Malawian Cameras
You're welcome to MalawianCameras
YouTube Channel Here we do these things
Reactions
News updates and commentary
Fun videos
Vlogging
So feel free to interact with with us
We need your wisdom and support
Let's build the world together with love and respect and peace
A Kamlepo Kalua akufusa mafusotu ku Judiciary ndipo akuti dzikoli tizitelo?
kodi ife timafuna tizikawapatsila nsimatu ku Waya nanga bwanji tikuwaonabe kunjaku a Mcpwa mwalusatu
Samuel Lwara Akuti ine ndili nganganga Chakwera amangidwe tikumufuna tikamfuse
JB wpabwera ndi Bible ndipo akuimba Gospel kungochoka Mcp maphuzo adasiya
Kwamereka kwaphedwa asilikali awiri ndipo Trump wati Cyril Ramaphosa asazabwere ku G20 yao 2026
Vitus Gregory Gondwe wabwerako paja anathawa kuMalawi Mcp ataiulura zakatangale wao
Samuel Lwara Akuti Chakwera yu Tam'mangeni pilizi apite akalowe tose tili naye milandu
Malawi nayo zopusa sifuna maiko omwe amatilipilitsa visa nao akamalowa m'malawi azilipira
Kukhalaku tisamakhalire Ndale zachimidzi ngati izi akuti makhansala akulemba azipani zao basi MCP
Mzinda wa Blantyre Amfumu Jomo akuyendera malo onyasa ndipo awauza anuwake Kuti izi ai
Kwavutatu Nde mwati Aba agalu ku State House?
Norman Chisale Ntchito mukugwira koma azipha dala anthu kuti muoneke olephera. Mada Mbewe
Ukraine yaimika manja mmwamba koma ikuphupha Pang'ono pankhani ya Malo
Manganya akuthandizabe anthu ngakhale kuti ndale zinatha koma pali wena akumuyamba dala
Magalimoto ang'ono ang'ono pa BIWI Pa Tank ku Lilongwe apeweni akuliza anthu
Billy Malata Wachemelera Mutharika? Akuti Amatha? Tisamangotsutsa zilizose? Eeeeee Malodza!!!!
Apa mwakwera iti? Misonkho ikwere kapena ai?
Achewa komaso mcp sizofanana amfumu achichewa akuti Gangata ndi one koma achewa ena akwiya
Awawa ndi achitatu kufuna kuberedwa munjira imeneyi Samalani
Mtsikana Wa Mcp kuchemelera Gangata? Ati Gangata ndi dolo? Tabwerezani pamenepo
Nkhani ya CDF Situation Malawi kwachemaa
Nkhani zitatu pomwe tatseka G20 Summit Cyril Ramaphosa wabweza chipongwe kwa Trump
Ati Achakwera Tisawalemekezeso ngati Pulezident opuma ndipo osawapasaso ndalama Namiwa kuseliku
Tiyeni Timvere limodzi paja uyutu amangoyankhula anasowa komatu....
Hot current 67 Billion a Mcp mwatani nayo???
South Africa yauza America ndi Trump kuti kagwere uko
Panazanvekako kuti Dpp imkasintha ma figala ku IMF ndi World Bank koma Denis Mahata wati nde Udolowo
Zandile Dabula President wa Operation Dudula amuthira utsi okhetsa msozi ndipo wakhaula wausilu
Ukuku nde Kutha kwa Ukraine basi Zelensky walira watsimikizaso Eti Trump wakweraso ya Putin eti.?