Sungani Mbewu Zanu Kuti ZIsaonongeke Pogwiritsa Ntchito Zibekete (Kontenala)
Автор: SAWBO™ Scientific Animations Without Borders
Загружено: 2025-10-22
Просмотров: 103
Sungani Mbewu Zanu Kuti ZIsaonongeke Pogwiritsa Ntchito Zibekete
(Kontenala)
Kanema uyu akufotokoza njira zomwe tingatetezere nyemba zathu ku
anankafumbwe pozisunga mu jerekani otsekedwa bwino. Kusunga
nyemba mjerekani monga tikuonera apa kungateteze nyemba kwa
nthawi yaitali. Tsono tionetsetse kuti tatseka bwinobwino kukamwa kwa
jerekaniyo.
Postharvest Loss: Hermetic Sealing with Locally Available Containers
in “Chichewa” (accent from “Malawi”)
This animation explains how to avoid insect damage when storing beans
after harvest using hermetically sealed containers. Beans can be stored
in a locally available, airtight container for long periods of time safely.
The container being used must be completely clean and free of any
contaminants. It can never have been used for any hazardous materials
such as fuel or pesticides.
Доступные форматы для скачивания:
Скачать видео mp4
-
Информация по загрузке: