JEG - Tonse || Dir. by M-Feli & SomeGuy
Автор: JEG tElLeM TV
Загружено: Дата премьеры: 25 мар. 2025 г.
Просмотров: 19 898 просмотров
#JegTellem #Mulungu #Gospel #afro #Malawimusic #2025 #JEG
Full Lyrics
TTT tElLeM
Yahman yah
Yah yah yah
JahJah amakonda tonse
Kuchoka mu nthawi ya Mose
Ndipake anatuma nkhoswe
Itiyang'anile izatisogoze
Komabe sitingakhonze zonse
Ubwino sitili nawo onse
Timapasidwa mwayi oti tikonze
Pomwe sifikila amayika Po step
Mulungu wathu ndi wamphavu
Wachifundo ndi Wa love
Olo tigone osadya
Iye amatizutsa kukacha
Mulungu wathu ndi wamphavu
Wachifundo ndi Wa love
Olo tigone osadya
Iye amatizutsa kukacha
Eh eh eh
Eh eh eh mhuu
Mbuye Ali nafe amakonda Tonse
Eh eh eh
Eh eh eh mhuu
Mavuto
Ndiwo apanga munthu
Sangaphe
Zatsogolo lathu
Poti chimwemwe ndi mtendere ndi zathu
Ndeno woyipayo sangapangepo kanthu
So one love is the language I chose
I'd care about the others if I was in their shoes
Kumasunga mangawa supindula kanthu
Ungozizunza wekha pokonda milandu
Mulungu wathu ndi wamphavu
Wachifundo ndi Wa love
Olo tigone osadya
Iye amatizutsa kukacha
Mulungu wathu ndi wamphavu
Wachifundo ndi Wa love
Olo tigone osadya
Iye amatizutsa kukacha
Eh eh eh
Eh eh eh mhuu
Mbuye Ali nafe amakonda Tonse
Eh eh eh
Eh eh eh mhuu
Mbuye all nafe amakonda tonse
Konda tonse eh
Konda tonse eh mhuu
Konda TOnse eh
Konda Tonse eh
Mhuu mhuu mhuu
Mulungu wathu ndi wamphavu
Wachifundo ndi Wa love
Olo tigone osadya
Iye amatizutsa kukacha
Mulungu wathu ndi wamphavu
Wachifundo ndi Wa love
Olo tigone osadya
Iye amatizutsa kukacha
Eh eh eh
Eh eh eh mhuu
Mbuye Ali nafe amakonda Tonse
Eh eh eh
Eh eh eh mhuu
Mbuye Ali nafe amakonda TOnse

Доступные форматы для скачивания:
Скачать видео mp4
-
Информация по загрузке: