Nkhani yamwana amene anathamangitsidwa mmudzi chifukwa chopha makolo Ake pobadwa
Автор: Kuwerenga ndi Brenda
Загружено: 2025-04-17
Просмотров: 30904
Mwamayu adamuthangitsa chifukwa anthu a mmudzi mwakwawo amati oye Ali ndi thembelero komanso nthakati. Mayi Ake adamwalira iye atangobadwa. bambo ake adamwaliranso tsiku lomwero. Agogo Ake adamwalira mwanayu Ali ndi zaka 10.
Nkhani ndiyopeka.
Доступные форматы для скачивания:
Скачать видео mp4
-
Информация по загрузке: