MFUMU YA ULEMELERO | Gawo 2 | KING of GLORY | Chichewa
Автор: KING of GLORY the Movie
Загружено: 2018-12-15
Просмотров: 5169
Gawo 1: • MFUMU YA ULEMELERO | Gawo 1 | KING of GLOR...
Gawo 2: • MFUMU YA ULEMELERO | Gawo 2 | KING of GLOR...
Ulendo wa mu Malemba a Aneneri umakuitanani inu kuti mukumane ndi Mfumu ya dziko komanso kumvetsa dongosolo lake lopulumutsa omutsatira oukira kuchokera ku ufumu wa mdima ndi kuwayenereza kukhala mu kuunika kwa Ufumu wake Muyaya.
Mofotokozeredwa kwa nzeru ndi zithunzi zokongongola kanema uyu ndi oyenera kwa anthu a dziko lonse ndi misikhu yonse.
Kanema yonse ndi ya mphindi 222, ndime 15, ndi magawo akulu awiri.
Gawo 1. Chipangano cha Kale: Mfumu kufotokozera dongosolo lake (ndime 1-8)
Gawo 2. Chipangano cha Tsopano: Mfumu Ikwanilitsa Dongosolo lake (Ndime 9-15)
MFUMU YA ULEMELERO: KHANI IMODZI MU NDIME 15
Gawo 1: Chpangano cha kale: Mfumu Ifotokozela Dongosolo Lake (Thawi: 1:47hrs)
1. Mawu oyamba (Ndime 1-3)
2. Mlengi ndi Zolengedwa zake (Ndime 4-9)
3. Kulowa kwa zoipa (Ndime 10-15)
4. Tembelero la Tchimo ndi Lonjezo la Mulungu (Ndime 16-19)
5. Njira ya Kupereka Sembe (Ndime 20-24)
6. Kuukira kwa munthu ndi Kukhulupirika kwa Mulungu
(Ndime 25-27)
7. Ndongosolo la Mulungu lipambana (Ndime 28-32)
8. Chilamulo ndi Aneneri (Ndime 33-36)
Gawo 2: Chipangano cha Tsopano: Mfumu ikwaniritsa dongosolo lake
9. Kulowa kwa Mfumu (Ndime 37-42)
10. Khalidwe la Mfumu (Ndime 43- 47)
11. Ulamuliro wa Mfumu (Ndime 48-51)
12. Cholinga cha Mfumu (Ndime 52-56)
13. Kugonjera kwa Mfumu (Ndime 57-61)
14. Nsembe ndi kupambana kwa Mfumu (Ndime 62-65)
Uthenga ndi Ulemelero wa Mfumu (Ndime 66-70)
Mulungu wathu Wamkulu (Yoimbidwa mu chi Arabu)
© 2019 ROCK International http://www.king-of-glory.com
This journey into the Scriptures of the prophets invites you to meet the one true God and understand His plan to rescue His rebellious subjects from the kingdom of darkness and qualify them to live with Him forever in His kingdom of light. With its thought-provoking narrative and inspired mix of animation and live video, this film is for a worldwide audience of all ages.
The full film is 222 minutes, grouped in 15 episodes, and divided into two main parts:
Part 1. Old Testament: The King Foretells His Plan {Episodes 1-8}
Part 2. New Testament: The King Fulfills His Plan {Episodes 9-15}
KING of GLORY: 1 STORY in 15 EPISODES
Part 1: Old Testament: The King Foretells His Plan [1 hour 47 minutes]
1. Prologue (Scenes 1-3)
2. The Creator & His Creation (Scenes 4-9)
3. Evil’s Entrance (Scenes 10-15)
4. Sin’s Curse & God’s Promise (Scenes 16-19)
5. The Way of the Sacrifice (Scenes 20-24)
6. Man’s Rebellion & God’s Faithfulness (Scenes 25-27)
7. God’s Plan Advances (Scenes 28-32)
8. The Law & the Prophets (Scenes 33-36)
Part 2: New Testament: The King Fulfills His Plan [1 hour 55 minutes]
9. The King’s Entrance (Scenes 37-42)
10. The King’s Character (Scenes 43-47)
11. The King’s Dominion (Scenes 48-51)
12. The King’s Mission (Scenes 52-56)
13. The King’s Submission (Scenes 57-61)
14. The King’s Sacrifice & Triumph (Scenes 62-65)
15. The King’s Gospel & Glory (Scenes 66-70)
How Great is Our God (Sung in Arabic)
Credits
© 2019 ROCK International http://www.king-of-glory.com
Доступные форматы для скачивания:
Скачать видео mp4
-
Информация по загрузке: