The Great Controversy 2.0 Project (Chichewa)
Автор: Alexs Studios
Загружено: 2022-09-20
Просмотров: 358
Nkangano Waukulu (The Great Controversy), ndi limodzi mwa mabuku apaderadera omwe Ellen G. White amafuna litagawidwa kwambiri.
Mogwirizana ndi khumbo limeneli, Forward for Christ Commission, FCC, bungwe loima palokha la utumiki mu mpingo wa Seventh-Day Adventist, Malawi Union Conference, lalowa nawo mu chochitika chomwe chikuchitidwa ndi mpingowu maiko ena, ndipo bungweli likufuna kugawa mabuku osachepera 7000 mu chaka cha 2023. Koma kuti izi zitheke, tifunika ndalama zosachepera MK9 Million.
Ngati mungafune kuthandiza nawo, tumizani thandizo lanu ku National Bank of Malawi, Acc. No. 1004717429, Forward for Christ Crusade, Central Region.
or Muimbireni Chiku Malopa +265 888 97 77 17. kapena Benson Singano +265 981 34 44 79, kuti mudziwe zambiri.
Forward for Christ Commission, Proclaiming the Everlasting Gospel.
Доступные форматы для скачивания:
Скачать видео mp4
-
Информация по загрузке: