Thanthwe-Roni Ginossar
Автор: רוני גינוסר - Roni Ginossar Official
Загружено: 2025-09-20
Просмотров: 334
Thanthwe
Music and lyrics : Precious Phiri
THANTHWE
Thanthwelo limbalo
Ndiye Yesu Khristuyo
Timwe madzi
Amoyo
Kuchoka Nthathwelo
Ati idzani Nonse
Olema ndi othodwa
Kuti Yesu alandire
Mavuto anuwo
Iye ndiwachifundo
He's a present help in trouble
Nanga bwanji mukungolila
Pothawira mulinapo
Ati Yesu Yesu Chitsime
Kasupe wa madzi amoyo
Inu Nonse onva ludzu, Yesu ndiye Mdambo
Yesu Yesu Kasupe
Kasupe wamadzi amoyo
Nanga bwanji mungolila pothawira muli napo
Mangani maziko
Olimbawo
Mangani banja lanu
Pa Yesu
Pamene mavuto adza banja silisweka
Koma mukamtsata Yesuyo
Simugwedezeka
להצטרפות לפייסבוק של רוני גינוסר:
/ ginossar
להצטרפות לאינסטגרם של רוני גינוסר:
/ roniginossar
Доступные форматы для скачивания:
Скачать видео mp4
-
Информация по загрузке: