Mic Mash - How Are You? ft. QUEST MW (Mental Health Short Film|Music Video)
Автор: Mic Mash
Загружено: 2025-06-18
Просмотров: 104243
Broken Crayons presents a mental health short film "How Are You? " featuring QUEST MW. Beat by waytoolost | Produced by Manifest | Shot and Edited by SeanyFilms | Script by Mic Mash | VFX by Matt The Creator #mensmentalhealth #mentalhealthawareness #mentalhealthmatters #mentalwellness #rap #mentaltoughness
Let's connect and follow me on all platforms
https://open.spotify.com/artist/7hzFi...
/ mic-mash
https://www.boomplay.com/share/artist...
https://www.deezer.com/en/artist/6855...
/ micmashmw
/ micmash265
/ micmash265
Lyrics
Chorus - Quest MW
Ndikudutsa nyengo zovutaaa
Mtima suli malo wangosuntha
Njala koma kufeelabe okhuta
Kusekelera ngati ndilibe zovuta
Ndikudutsa nyengo zovutaaa
Mtima suli malo wangosuntha
Njala koma kufeelabe okhuta
Kusekelera ngati ndilibe zovuta
Akandifunsa how are you ?
I’m okay
how are you ?
I’m okay
Akandifunsa how are you ?
I’m okay
how are you ?
I’m okay
Verse 1 - Mic Mash
Akandifunsa how are you uh uh
Moyo ukuyenda one two uh uh
Loner sindikonda Anthu uh uh
Zimathela mu mtima mwathu uh uh
Ndikudutsa Nyengo zowawa
Daily kungokhalira bawa
Nkhawa, inu kuno ntchito zikusowa
Kuyembekeza mawa koma nthawi ikuthawa
Ambuye ine bwanji mungodalitsa enawa
Ndikukula Panopa ndili pa pressure
Zokolola kulibe koma tafesa
Chichilichonse ndi nthawi eya ndamvetsaaaa
Mukandikweza mungochotsa zonse zogwetsa
Undipeza kupemphetsa kuma page ama biggy
Ndine top fan konseko nde andi bigge
Ukandifunsa how are you ?
Ndimayankha im okay kuti zithe
Chorus - Quest MW
Ndikudutsa nyengo zovutaaa
Mtima suli malo wangosuntha
Njala koma kufeelabe okhuta
Kusekelera ngati ndilibe zovuta
Ndikudutsa nyengo zovutaaa
Mtima suli malo wangosuntha
Njala koma kufeelabe okhuta
Kusekelera ngati ndilibe zovuta
Akandifunsa how are you ?
I’m okay
how are you ?
I’m okay
Akandifunsa how are you ?
I’m okay
how are you ?
I’m okay
Verse 2 - Mic Mash
Osabisa tandiyankhe vhilungamo how are you?
Ukubisa nkhawa zako ndaonela bawa yu
Sangakupatse nkhondo yoti sungaimalize
Sangakupatse ntchito yoti sungaikwanitse
If I tell you I’m not okay ndiwe nzanga
Ndigwile nkono ndikukonza life yanga
Fake it till you make it ndi mental health yanga
Mamuna salira depression imalanga
You want me to open up, mukumandiseka
Chikangokhala kwa nzako ndi pomwe chimaphweka
Just a reminder, broken crayons they still color
Mdima ungakule bwanji kuzabwela so kuwala
Chorus - Quest MW
Ndikudutsa nyengo zovutaaa
Mtima suli malo wangosuntha
Njala koma kufeelabe okhuta
Kusekelera ngati ndilibe zovuta
Ndikudutsa nyengi zovutaaa
Mtima suli malo wangosuntha
Njala koma kufeelabe okhuta
Kusekelera ngati ndilibe zovuta
Akandifunsa how are you ?
I’m okay
how are you ?
I’m okay
Akandifunsa how are you ?
I’m okay
how are you ?
I’m okay
Outro - Mic Mash & QUEST MW
Osamangoti uli bhoo
It’s good to open up to somebody
Be real, be heard
Take care of your mental health
How are you ?
How are you ?
How are you ?
How are you ?
How are you ?
How are you ?
Yaaaaaaaaaaah
Доступные форматы для скачивания:
Скачать видео mp4
-
Информация по загрузке: