Kuyakhula kwa Precious kabambe
Автор: PBW STUDIO
Загружено: 2025-06-16
Просмотров: 51
Yemwe akufuna kuyimira ngati phungu wa nyumba ya malamulo ku dera la Bwaila ku Lilongwe a Precious Ufulu Kabambe ati zomwe bungwe la AQSA lachita popera makina osokera kwa amai zithandiza kuti anthu derali akhale idziimira pa okha.A Kabambe ati a mabungwe ali ndi udindo wothandiza anthu ndi zinthu zosiyana siyana monga momwe bungwe la AQSA lachitira.Phunguyu wanena izi lamulungu pomwe bungwe la AQSA lachisilamu limapereka masatifiketi komaso makina osokera okwana 50 kwa amai omwe amaliza maphunziro osoka pa sukulu ya Mai Fatima kwa Chinsapo.A Kabambe ati mayiwa adala polandira makiwa ndipo awasamalire kuti athandize miyoyo yawo."Tiwathokoze a AQSA kaamba ka thandizoli, izi zithandiza amai athu kukhala odzalira okha, izi ndi zomwe mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera akulimbilitsa", anatero a Kabambe.Amayi okwana 50 ndi omwe amaliza maphunziro osoka pa sukuluyi pomwe ena okwana 100 sanamalize maphunziro awo.#Blessings Chikoti PBWtv Lilongwe 16/06/2025Yemwe akufuna kuyimira ngati phungu wa nyumba ya malamulo ku dera la Bwaila ku Lilongwe a Precious Ufulu Kabambe ati zomwe bungwe la AQSA lachita popera makina osokera kwa amai zithandiza kuti anthu derali akhale idziimira pa okha.A Kabambe ati a mabungwe ali ndi udindo wothandiza anthu ndi zinthu zosiyana siyana monga momwe bungwe la AQSA lachitira.Phunguyu wanena izi lamulungu pomwe bungwe la AQSA lachisilamu limapereka masatifiketi komaso makina osokera okwana 50 kwa amai omwe amaliza maphunziro osoka pa sukulu ya Mai Fatima kwa Chinsapo.A Kabambe ati mayiwa adala polandira makiwa ndipo awasamalire kuti athandize miyoyo yawo."Tiwathokoze a AQSA kaamba ka thandizoli, izi zithandiza amai athu kukhala odzalira okha, izi ndi zomwe mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera akulimbilitsa", anatero a Kabambe.Amayi okwana 50 ndi omwe amaliza maphunziro osoka pa sukuluyi pomwe ena okwana 100 sanamalize maphunziro awo.#Blessings Chikoti PBWtv Lilongwe 16/06/2025
Доступные форматы для скачивания:
Скачать видео mp4
-
Информация по загрузке: