Malumbo Harawa's inspiring story - Dial 460 then select 1 to vote for Malumbo.
Автор: Airtel Malawi
Загружено: 2023-05-21
Просмотров: 283
Malumbo akuthandiza antchito za umoyo pogwiritsa luso lake kukhonza makina osiyana siyana amu zipatala monga ma oxygen concentrator ndi zipangizo zina mwaulere.
Ngati nkhani ya Malumbo yakukhudzani, mupatseni chilimbikitso.
𝐈𝐦𝐛𝐚𝐧𝐢 𝟒𝟔𝟎, 𝐒𝐚𝐧𝐤𝐡𝐚𝐧𝐢 𝟏 𝐤𝐮𝐭𝐢 𝐦𝐮𝐯𝐨𝐭𝐞𝐥𝐞 𝐌𝐚𝐥𝐮𝐦𝐛𝐨 𝐇𝐚𝐫𝐚𝐰𝐚.
#ZiliMwaIfe #MalawiAdaliraInu #Votenow
Доступные форматы для скачивания:
Скачать видео mp4
-
Информация по загрузке: