UDF Sizalowaso M’Boma - DMD
Автор: Nyasa VoiceBox
Загружено: 2025-12-09
Просмотров: 214
On Nyasa VoiceBox, DMD says the United Democratic Front (UDF) will never rule Malawi again, adding that Malawians should remember that many of the challenges the country faces today began during the UDF era.
Pa Nyasa VoiceBox, DMD yati chipani cha United Democratic Front (UDF) sichidzalamuliranso dziko la Malawi, ndipo akuti Amalawi akumbukire kuti mavuto ambiri omwe dzikoli likukumana nawo lero zinayamba nthawi ya UDF.
#malawi #udf #africa #politics
Доступные форматы для скачивания:
Скачать видео mp4
-
Информация по загрузке: