Estiner Katengeza -Zokoma ndi Zakuyanja (Lyric video)
Автор: Estiner Katengeza
Загружено: 2022-12-29
Просмотров: 18026
Declare along that goodness and mercy follow you
Intro
Zokoma, Zoyanja
Zokoma, Zoyanja
Verse 1
(Zokoma ndi Zakuyanja zimanditsata ine) x2
(Everything is alright)x3
Zanga zimayenda
(Malire a Yehova pa moyo wanga
Anagwera pabwino)x2
When I look to the left
Everything is alright
When I look to the right
Everything is alright
Lero langa, mawa langa
Pansi pano ndi kumwambanso
Changa ndi ichichi
Yahweh Wandipatsa
Anga ndi awawa
Yahweh Wandipatsa
Cholowa changa ichichi
Yahweh Wandipatsa
Wanga ndi uwuwu
Yahweh Wandipatsa
He eh, he eh
Yahweh Wandipatsa
He eh, he eh
Yahweh Wandipatsa
Verse 2
Ntchito za manja anga
Nzodalitsika
Ine kulowa kwanga
Nkodalitsika
Olo kutuluka kwanga
Nkodalitsika
Ah he eh eh
Zanga zimayenda
Ndikakhala pa nyumba
Zanga zimayenda
Ndikayenda kwao kwa azungu
Zanga zimayenda
Ngakhale kwathu kuno ku Malawi
Zanga zimayenda
Zanga ndi izizi
Yahweh Wandipatsa
Anga ndi awawa
Yahweh Wandipatsa
Cholowa changa ichichi
Yahweh Wandipatsa
Umboni wanga uwuwu
Yahweh Wandipatsa
Verse 3
Londo londo londo
Zokoma ndi Zakuyanja zimanditsata ine
Londo londo londo
Zokoma ndi Zakuyanja zimanditsata ine
When I look to the left
Everything is alright
When I look to the right
Everything is alright
Lero langa, mawa langa
Pansi pano ndi kumwambanso
When I look to the left
Everything is alright
When I look to the right
Everything is alright
Lero langa, mawa langa
Pansi pano ndi kumwambanso
Londo londo londo
Zokoma ndi Zakuyanja zimanditsata ine
Londo londo londo
Zokoma ndi Zakuyanja zimanditsata ine
Londo londo londo
Zokoma ndi Zakuyanja zimanditsata ine
Londo londo londo londo eh!
Zokoma ndi Zakuyanja zimanditsata ine
Outro
Zokoma, Zoyanja
Londo londo, kunditsata
Zokoma, Zoyanja
produced by OBK Beatz
Доступные форматы для скачивания:
Скачать видео mp4
-
Информация по загрузке: