Crispy Malawi Ndi Abale Athu Official Music Film
Автор: Crispy Malawi
Загружено: 2023-08-06
Просмотров: 69752
Ndi Abale Athu Music Film
produced by Famous
Shot By Lincon
Edited By KUlair
Colorist Kulair
Casting
K1 $mollet
wylie Famous Chilunga
Upile Johnson
Alex Tyga Chirwa
Farliz Fracisco Lucas
Yamanata
Apolice ndi A Bale Athu x 8
(Post Chorus)
Kupeza Money ndi u Shasha
Ndine street smart Hustler
With my Self Made kwacha
Blessings kuno ndiku Mtaja x2
40pin kuipanga ikhale 80pin
Sizikufunika Degree
Ndiza Straight can’t you See?
UngoikaFocus
Umve zomwe ndikunenazi
Anthu ndi Ama Jelousy
Uka ma Chaser zi paper zi
Rule # 1
Be your self don try to Be me
Uka Burna ka Cannabis
Kosala uzikabisa
Be Your Plug
Cut off your Middle man
Ma Move amadhulisa
Basi maluzi taakhaulitsa
Verse 2
Kukonda ku woker figure ku Hita G spot
Hustle imayamba aka hitta record
Iiih Ukufuna Beef ase eko T bone
Ndafika ndi stainado Wachika ku CICOD
Spe ndi King of The ghetto fredo ndi ghetto king kong
funa kupanga Billi kuvutisa ku ding dong
Nyimbo zolemba ku ma Message pano ndima Rington
Ma Verse angozaza funa ndipeze Vepi ku Synod
Gist yako ipeze vep ine Ndilibe Nayo ntchito
She’s in my bed after iwe kumutengera pa Galitos
Uma Trappa ndima Chick koma onunkha zitosi
Ndili mmutu mwama Diva ngati ribbon 🎀
Ndangotulusa Chida weapon
Ife Ndi Amalawi Ent. 2023
Доступные форматы для скачивания:
Скачать видео mp4
-
Информация по загрузке: