Amene Akudana Ndi Zoti Ma MP Asamagwile CDF Amene Amdana Ndi Dziko – Silrage Phiri
Автор: Nyasa VoiceBox
Загружено: 2025-11-27
Просмотров: 339
On Nyasa VoiceBox, Mr. Silrage Phiri says anyone opposing the Constitutional Court ruling that Members of Parliament should have no role in managing Constituency Development Funds (CDF) is an enemy of progress for Malawi and Malawians.
Pa Nyasa VoiceBox, a Mr. Silrage Phiri ati aliyense yemwe akutsutsa chigamulo cha Khoti la Malamulo chakuti Mamembala a Nyumba ya Malamulo asalowererepo pa kasamalidwe ka Constituency Development Funds (CDF) ndi mdani wa chitukuko cha Malawi ndi a Malawi.
#malawi
Доступные форматы для скачивания:
Скачать видео mp4
-
Информация по загрузке: