Nkhani ya Oimba Band a Eli Njuchi Mizimu yao iwuse Muntendere...
Автор: Malawian Cameras
Загружено: 2025-12-26
Просмотров: 10730
In moments like these, it’s easy for noise to rise and stories to be twisted.
Koma nthawi ngati izi, tifunika kuleza mtima, kumvetsetsa, ndi chifundo, osati mawu ochuluka.
This is not just about a show or music plans.
Izi ndi za moyo, ubale, ndi anthu amene anali gawo lofunika pa ulendo wautali. Zomwe zachitika zapweteka kwambiri, osati kwa munthu mmodzi basi, koma kwa nyimbo za ku Malawi zonse.
Stay strong, ELI Njuchi .
Anthu omwe atisiya sanali kungokhala band members, koma abale, anzathu, ndi anthu amene munamangira limodzi maloto ndi tsogolo. Ululu umenewu ndi weniweni, ndipo dziko lonse likumvetsa kupweteka kumeneku.
As a country, tili nanu pa nthawi yovuta imeneyi.
Tikusankha kuyima nanu, osati kuweruza. osati kulankhula kwambiri.
Mulungu apumitse mizimu ya omwe atisiya,
ndipo apatse mphamvu ndi mtendere mabanja onse omwe akukhudzidwa. 🕊️🤍
Malawi ili nanu. RIP
—
Доступные форматы для скачивания:
Скачать видео mp4
-
Информация по загрузке: