Популярное

Музыка Кино и Анимация Автомобили Животные Спорт Путешествия Игры Юмор

Интересные видео

2025 Сериалы Трейлеры Новости Как сделать Видеоуроки Diy своими руками

Топ запросов

смотреть а4 schoolboy runaway турецкий сериал смотреть мультфильмы эдисон
dTub
Скачать

Khalabe Odikira - The Morning Star (Official Video)

Автор: The Morning Star - Mw

Загружено: 2023-10-20

Просмотров: 344247

Описание:

Lyrics:
1. Zosautsa zochuluka okondedwa m'moyowu
Kukumana ndi zipsinjo zosaneneka
Kuyesetsa kupemphera ngati Mlungu saakumva
Zafika povuta moyuwu kuwawa

Kuyang’ana uko wachoka ndizogwetsa mphwayi
Kuganiza zatsogolo mtima umasweka
Nthawi zina ukaona ena zithu zikuwayendera
Zimangopangitsa ‘we kukhumudwa

Chorus
Kaya nyengo ivute iwopse bwanji
Ndi zinthu za kanthawi kanthawi kochepa
Zisakuchotse ‘we pamaso pa Mulengi wako
Khalabe odikira mkhulupire

Akulonjeza kukhala nawe kukusamalira zinthu zikavuta
Ngakhale lonjezano lake lichedwe bwanji
Khalabe odikira mkhulupire

2. Zolilitsa tsiku ndi tsiku kuopsedwa m'moyowu
Kunyozedwa ndiopembedza nao limodzi
Komabe m'nyengo zotere kumbuka liripo bwenzi
Bwenzi lopambana ndiye Yesu

Akhala nawe poyenda akhala nawe pogona
Akhala mawe mtendere ndinso polira
Iye ali ndi chinsisi cha tsogolo la moyo wako
Khalabe odikira mkhulupire
-----------------------------------------------------
The Morning Star, Kawale, Lilongwe
Audio by: Recall, Kuimba Mwamphamvu Studio
Video by: Hope Channel Malawi
-----------------------------------------------------
Share this video:
   • Khalabe Odikira - The Morning Star (Offici...  

Subscribe for more videos:
   / @themorningstar-mw  

Audio playlist:
   • M'bandakucha Album - The Morning Star  
-----------------------------------------------------
Connect with us:
Facebook:   / themorningstarsingersmw  
Instagram:   / themorningstar_mw  
Whatsapp: https://whatsapp.com/channel/0029Va5V...
Spotify - https://spotify.link/EC6GyW0v3xb

E-mail:
themorningstarsingers@gmail.com

Khalabe Odikira - The Morning Star (Official Video)

Поделиться в:

Доступные форматы для скачивания:

Скачать видео mp4

  • Информация по загрузке:

Скачать аудио mp3

Похожие видео

N'dzakondwa - Alex Mandala

N'dzakondwa - Alex Mandala

Джем – Khalabe Odikira - The Morning Star (Official Video)

Джем – Khalabe Odikira - The Morning Star (Official Video)

DIKILANI (official video)

DIKILANI (official video)

MPHAMVU YA KUMWAMBA - Pastor TY Nyirenda// CHIRIMBA Camp Meetings

MPHAMVU YA KUMWAMBA - Pastor TY Nyirenda// CHIRIMBA Camp Meetings

Naaman_DORCAMO

Naaman_DORCAMO

Джем – The Morning Star

Джем – The Morning Star

Msonkhano Wa Kale - The Morning Star (Official Video)

Msonkhano Wa Kale - The Morning Star (Official Video)

SATANA AMABWELA KUDZAYESA CHOONA CHATHU

SATANA AMABWELA KUDZAYESA CHOONA CHATHU

Ambassadors of Christ ft Mwalimu Ssozi Joram ||Best Performance in Uganda

Ambassadors of Christ ft Mwalimu Ssozi Joram ||Best Performance in Uganda

Udandaulanji - The Morning Star (Official Video)

Udandaulanji - The Morning Star (Official Video)

Florence Massea - Mpulumutsi Wozizwitsa ndi Yesu (official lyric video)

Florence Massea - Mpulumutsi Wozizwitsa ndi Yesu (official lyric video)

N'DZIYAMIKA_ GOSPEL CARRIERS_ SDA MALAWI MUSIC COLLECTIONS

N'DZIYAMIKA_ GOSPEL CARRIERS_ SDA MALAWI MUSIC COLLECTIONS

Nthandizeni. Alex Mandala

Nthandizeni. Alex Mandala

Anthu adzalowa kuchipinda kwanu || Rev Yasin Gama

Anthu adzalowa kuchipinda kwanu || Rev Yasin Gama

Machenjerero A Farawo  || Pastor TY Nyirenda Msonkhano Wamisasa Wapakanema -Tsiku Lachiwiri (Day 2)

Machenjerero A Farawo || Pastor TY Nyirenda Msonkhano Wamisasa Wapakanema -Tsiku Lachiwiri (Day 2)

Ambassadors of Christ Choir - INDIRIMBO NZIZA ZIRYOHEYE AMATWI (Best Playlist 2025)

Ambassadors of Christ Choir - INDIRIMBO NZIZA ZIRYOHEYE AMATWI (Best Playlist 2025)

Sanctuary Hymns 😘English versions🙏#sda #ghanaentertainment #acapella #acapeldridge

Sanctuary Hymns 😘English versions🙏#sda #ghanaentertainment #acapella #acapeldridge

The Great Angels Choir - Wake wake (Official Music Video)

The Great Angels Choir - Wake wake (Official Music Video)

Wanandi Wakusowa Mtende Official Video By Chiputula Umodzi AC Choir

Wanandi Wakusowa Mtende Official Video By Chiputula Umodzi AC Choir

Namasalima Singers  | Adzayankha

Namasalima Singers | Adzayankha

© 2025 dtub. Все права защищены.

  • Контакты
  • О нас
  • Политика конфиденциальности

Контакты для правообладателей: infodtube@gmail.com