Udandaulanji - The Morning Star (Official Video)
Автор: The Morning Star - Mw
Загружено: 2025-12-31
Просмотров: 1609
Philippians 4:6 (NKJV)
"Be anxious for nothing, but in everything by prayer and supplication, with thanksgiving, let your requests be made known to God."
-----------------------------------------------------
Udandaulanji?
Udandaulanji? Udelanji nkhawa?
Ngati ulibe Mpulumutsi?
Mabvuto azinga, zinthu sizi 'yenda,
Ulibenso choti ungachite.
CHORUS
M'malo modandaula za mabvuto ako,
Uwuze mabvuto ako uli ndi Yesu
Amakukonda, amasamala 'we
Adzabisa 'we mumapiko ake.
Ngati mwana wanu atapempha mkate,
Ndani kodi angampatse mwala?
Tipatsa ana athu zinthu zabwino,
Kulibwanji 'Tate wathu woyera?
Eeh sitiri tokha ngati amasiye,
Mbuye alinafe nthawi zones.
Adanena kale adzasamala ’fe,
Kufikira chimaliziro.
-----------------------------------------------------
Share this video:
• Udandaulanji - The Morning Star (Official ...
Subscribe for more videos:
/ @themorningstar-mw
-----------------------------------------------------
Connect with us (subscribe and follow):
Facebook: / themorningstarsingersmw
Instagram: / themorningstar_mw
Tiktok: / themorningstar_mw
Whatsapp: https://whatsapp.com/channel/0029Va5V...
Spotify - https://spotify.link/EC6GyW0v3xb
Доступные форматы для скачивания:
Скачать видео mp4
-
Информация по загрузке: